Notice to FMB & OIBM customers

By Published On: October 31st, 2017Categories: News

CLOSURE OF BRANCHES / AGENCIES & INTERRUPTION OF SERVICES ON 4TH NOVEMBER, 2017

Please note that all branches and agencies of FMB and OIBM will be closed on Saturday 4th November, 2017 to enable us to migrate OIBM operations to FMB Bank.

Please note that Banki M’manja (mobile phone transactions) and ATM cards of OIBM customers will not work from 6:00 pm on 3rd November, 2017 to 11:00 am on 5th November, 2017, due to system migration procedures.

In addition services on FMB ATMs, POS’ and First Mobile will also be interrupted from 12.00 midnight on Saturday 4th November to 06.00am on 5th November, 2017.

We regret any inconvenience the above unavoidable migration will cause, and request patience and cooperation from all existing OIBM customers.

For any queries please contact 8000 3300 (toll free from TNM #s), 01 830 000 (toll free from MTL #s) or 01 832 508 (from other numbers) or via email at [email protected]

Or 4000 (toll free from TNM #s), 400 (toll free from Airtel #s) and 0111 912 162 (toll free from MTL #s) or via email at [email protected]

FMB / OIBM MANAGEMENT


CHIDZIWITSO KWA MAKASITOMALA A FMB NDI OIBM

KUTSEKA KWA MABANKI A FMB NDI OIBM NDI NCHITO ZAWO PA 4 NOVEMBALA, 2017

Chonde dziwani kuti nthambi zonse zamabanki a FMB ndi OIBM zizakhala zotseka loweruka pa 4 Novembala chaka chino pomwe mabankiwa azakhale akukhazikitsa ndondomeko zoti akhale banki imodzi.

Paichi dziwani kuti nchito zina zabanki ya OIBM kudzera njira zina monga makina aATM, maPOS ndi Mafoni a (Banki M’manja) zizakhala zisakugwira ntchito kuyambira nthawi ya 6 koloko madzulo pa 3 Novembala, kufikira nthawi ya
11 koloko m’mawa pa 5 Novembala 2017.

Ntchito zina za banki ya FMB pamakina a ATM, POS ndi Intaneti kuphatikizapo First Mobile (kugwiritsa ntchito foni ya’manja) sizizapezeka kuyambira 12.00 koloko yausiku loweruka pa 4 Novembala kukira 06.00 koloko m’mawa lamulungu pa 5 Novembala, 2017.

Tikupepesa chifukwa cha chakusapezeka kwa ntchito zathuzi pakanthawi kochepaka ndipo tikukupemphani kuti mukhale omvetsesa.

Kuti mudziwe zambiri imbani: 8000 3300 (mwaulele mukaimba kuchokera panambala ya TNM), 01 830 000 (mwaulele mukaimba kuchokera panambala ya MTL), kapenanso 01 832 508 kapena tumizani imelo ku [email protected]

Muthanso kuimba ku OIBM panambala izi mwaulere: 4000 (TNM), 400 (Airtel) ndi 0111 912 162 (MTL) kapenanso kutumiza imelo ku [email protected], mpaka pa 3 Novembala 2017.

UTHENGAWU WACHOKERA KUMABANKI A FMB NDI OIBM

FMBcapital Holdings Plc (FMBCH.mw)

Share price: 10,801.00 Tambala (0.00 | 0.00% – 10/08/22)

Sign up for Email Alerts

Recent Documents & News